Starise Furniture & Home Decor

Starise Furniture & Home Decor We are in Lilongwe near cashbuild Orange building opposite Malawi Housing shop #7 where there is Malawi housing

Thank you partner Max & Sherry Dine and Lounge ndi ma partner onse one mukuonetsa love ku STARISE
13/05/2026

Thank you partner Max & Sherry Dine and Lounge ndi ma partner onse one mukuonetsa love ku STARISE

Congratulations kwa onse omwe apata tray yokongolayi kutengera engagement yawo pa page pathu week imeneyi(weekly engagem...
09/05/2026

Congratulations kwa onse omwe apata tray yokongolayi kutengera engagement yawo pa page pathu week imeneyi(weekly engagement list yomwe facebook yatipatsa) Madalitso Majiya
Chisomo Nyirenda Nyakaunga Misozi Chirwa and Beatrice Zingwangwa I will add the 6th one for being the first one to tag the products she got from our shop Maggie Msiska mwakwana pitilizani kuikonda STARISE nonse.

Kuti mutenge tray yanu imbani

0999629159 or visit our shops in area 4 near Cashbuild pomwe pali sunset funeral services shop #7 or kapena Fikani ku work shop yathu ku gulliver nsewu wa Babtist mukamapita ku Padre pio pa hump yachiwiri kumanja

Mwadzuka bwanji ma partner. Lero anthu 5 apite ndi ma tray 5 okongolawa tingatengere chani popereka kwa oikonda STARISE.
09/05/2026

Mwadzuka bwanji ma partner. Lero anthu 5 apite ndi ma tray 5 okongolawa tingatengere chani popereka kwa oikonda STARISE.

Mpando Uwu ainiake anvekere ndimafuna ndingoutaya ife Tati komatu tikhoza kuukonza muzaudabwa. Sanakhulupilire kuti unga...
08/05/2026

Mpando Uwu ainiake anvekere ndimafuna ndingoutaya ife Tati komatu tikhoza kuukonza muzaudabwa. Sanakhulupilire kuti ungaoneke chonchi nanuso Tabweretsani wanu usandulike. Mitengo imatengera design ndi nsalu yomwe mukufuna. Mwakoma nonse

Phone 📞 0999629159

08/05/2026

Partner yemwe anabwera ku shop kwathu kugula set ya Mpando lero this morning apart from discount yomwe takupatsani mubwere muzatenge ma cushion covers 5 aulere mpando ukawale.

MaxSherians you are the best partnership ikuyenda bwino Kwambiri 😍

Taonani taonani mipando ina mwa mipando yonse tinasintha 🥰🥰
08/05/2026

Taonani taonani mipando ina mwa mipando yonse tinasintha 🥰🥰

Kodi mukudziwa kuti ife ndife akatswiri okonza mipando yakale kukhalanso yatsopano. Ngakahale kusintha deisgn zimatheka....
08/05/2026

Kodi mukudziwa kuti ife ndife akatswiri okonza mipando yakale kukhalanso yatsopano. Ngakahale kusintha deisgn zimatheka. Mitengo imatengera design yanu. Tatiyeseni simuzakhumudwa

Lilongwe

Phone 📞 0999629159

Ma set a clean osamba. Mk400000 umodzi zatengeni. Mukambirane kulipo Tiyankhuleni pa 0999629159
07/05/2026

Ma set a clean osamba. Mk400000 umodzi zatengeni. Mukambirane kulipo

Tiyankhuleni pa 0999629159

Tikuthokoza onse amene amapanga share ma post athu. We don’t take it for granted. Christina Wa Mike Banda ndi Mphatso Mu...
06/05/2026

Tikuthokoza onse amene amapanga share ma post athu. We don’t take it for granted. Christina Wa Mike Banda ndi Mphatso Muliya ndi Emmily Makina kwa week ino inu atatu mwapanga share ma post athu Kwambiri muzatenge flower pot imodzi imodzi ku shop kwathu 🥰🥰

Tangoyesani kupeza iti mukaike pa mpando pa living room panu mukaone kuwala kwake. Zosaboola mthumba izi. Prices are for...
06/05/2026

Tangoyesani kupeza iti mukaike pa mpando pa living room panu mukaone kuwala kwake. Zosaboola mthumba izi.

Prices are for covers only

Fikani shop yathu ili mu area 4 Chimambula pafupi ndi Cashbuild orange building opposite Malawi housing shop #7

Phone 0999629159

Google Map: https://maps.google.com/?q=-13.974011,33.776131

Zagule flower pot partner nyumba ikongole 🥰🥰 mitengo ili pa ma photos pomwepo.Tipezeni ku Lilongwe area 4 Chilambula paf...
05/05/2026

Zagule flower pot partner nyumba ikongole 🥰🥰 mitengo ili pa ma photos pomwepo.

Tipezeni ku Lilongwe area 4 Chilambula pafupi ndi Cashbuild power pali Sunset funeral services shop #7

0999629159

Address

Babtist Church
Lilongwe Area 18

Telephone

+265999629159

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Starise Furniture & Home Decor posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Starise Furniture & Home Decor:

Share