Zayn Cement Blocks and Mobile Service

Zayn Cement Blocks and Mobile Service This is a blick laying company that specializes in molding cement blocks. We are situated in Mzuzu, Malawi and we travel to places upon booking.

Prices are charged upon a dialogue with the customer. Contact us on 0996469915 for more info.

Mukafuna ma cement blocks olimba, tipedzeni ifeyo a Zayn Cement Blocks ndipo simudzakhumudwa. Mtengo ndi okambilana. Muc...
24/09/2024

Mukafuna ma cement blocks olimba, tipedzeni ifeyo a Zayn Cement Blocks ndipo simudzakhumudwa. Mtengo ndi okambilana. Muchedweranji ife tilipo?

Zayn mobile service ikuthokoza kwa onse amene akupeza ma blocks ku kampani imeneyi motelo asisilathu mitengo yama servic...
23/08/2024

Zayn mobile service ikuthokoza kwa onse amene akupeza ma blocks ku kampani imeneyi motelo asisilathu mitengo yama services yawoyose, bwelani popeza zabwino sizichedwa kutha axanu akutenga

Ngati mukufuna ma cement blocks olimba, tipedzeni ndipo simudzakhumudwa. Timakafika kulikonse komwe mukufuna kuti tikagw...
05/08/2024

Ngati mukufuna ma cement blocks olimba, tipedzeni ndipo simudzakhumudwa.

Timakafika kulikonse komwe mukufuna kuti tikagwire ntchito ndipo mtengo ndi okambilana. Tikupedzeka mu mzinda wa Mzuzu koma mukafuna kumva zambiri, imbani phone pa 0996469915.

Address

Mzuzu

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Zayn Cement Blocks and Mobile Service posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share