Mukani Building Contractors and Furniture

Mukani Building Contractors and Furniture Carpentry, Joinery & Furniture Contractors

19/01/2023

Amalawiiii!!!! Ife a Mukani Building Contractor Tabwelaso muchaka chino ndi mitengo yontchiiipa kwambiri poganizila mmene ndarama ikuvutila mwiyi uwu choooonde usakuphonyeni timbileni phone lero pama number awa 0994123894 kapena WhatsApp yokha pa 0884612317

Muli ndi nyumba yofuna denga labwino
Mukufuna Muike ceiling mnyumba mwanu
Mukufuna mumange upstairs nde mukufuna carpentry work ngati decking, Shuttering
Komanso ma maintenance onse okhunza carpentry tiuzeni lero ife nde madolo ake

Call us on 0994123894 calls only
WhatsApp only 0884612317

We are in located at sunside

Address

Blantyre

Telephone

+265994123894

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Mukani Building Contractors and Furniture posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Mukani Building Contractors and Furniture:

Share